LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb19 April masa. 4-5
  • Kodi Mudzakonzekela Bwanji Cikumbutso?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kodi Mudzakonzekela Bwanji Cikumbutso?
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
  • Nkhani Zofanana
  • Ndandanda ya Kuŵelenga Baibo pa Nyengo ya Cikumbutso ca 2023
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Ndandanda ya 2022 ya Kuŵelenga Baibo pa Nyengo ya Cikumbutso
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Ndandanda ya Kuwelenga Baibulo pa Nyengo ya Cikumbutso ca 2025
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2025
  • Ndandanda ya Kuŵelenga Baibo pa Nyengo Ya Cikumbutso ca 2024
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku Misonkhano—2024
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
mwb19 April masa. 4-5

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Kodi Mudzakonzekela Bwanji Cikumbutso?

Kuyambila caka cino, tidzayamba kukhala na nthawi yoculuka yokonzekela Cikumbutso ca imfa ya Khristu. Ngati Cikumbutso cacitika mkati mwa wiki, Msonkhano wa Umoyo na Utumiki, suzikhalako. Komanso, nkhani ya anthu onse na Phunzilo la Nsanja ya Mlonda, kuzikhala kulibe ngati Cikumbutso cacitika pa wikendi. Kodi mudzaseŵenzetsa nthawi imeneyi mwanzelu pokonzekela Cikumbutso? Monga mmene zinalili m’nthawi ya atumwi, makonzedwe afunika kupangidwa okhudza cocitika capadelaci. (Luka 22:7-13; km 3/15 1) Koma tonsefe tifunika kukonzekeletsa mitima yathu. Tingacite bwanji zimenezi?

  • Ganizilani ubwino wopezekapo.—1 Akor. 11:23-26

  • Pemphelani na kuganizila mmene ubwenzi wanu ulili na Yehova.—1 Akor. 11:27-29; 2 Akor. 13:5

  • Ŵelengani na kusinkha-sinkha Malemba amene akamba za tanthauzo la Cikumbutso.—Yoh. 3:16; 15:13

Ofalitsa ena amaŵelenga na kusinkha-sinkha Malemba a pa nyengo ya Cikumbutso opezeka m’kabuku ka Kusanthula Malemba Tsiku na Tsiku. Ena amaŵelenga Malemba amene ali pa chati imene ili pansipa. Enanso amaŵelenga nkhani za m’maganizini a Nsanja ya Mlonda zokamba za Cikumbutso na cikondi cimene Yehova na Yesu anatisonyeza. Njila iliyonse imene mungasankhe, idzakuthandizani kuyandikila kwambili Yehova na Mwana wake.

Wiki Yothela ya Moyo wa Yesu Padziko Lapansi (Mbali 1 na 2)
    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani