LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 March tsa. 15
  • Zisankho Zimene Zimaonetsa Kuti Timadalila Yehova

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Zisankho Zimene Zimaonetsa Kuti Timadalila Yehova
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Kufuna-funa Nzelu mwa Kuŵelenga Baibo Tsiku Lililonse
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Lembani Mmene Mwapitila Patsogolo
    Citani Khama pa Kuŵelenga na Kuphunzitsa
  • Pangani Zisankho Zokondweletsa Yehova
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2025
  • Zimene Tiphunzilapo pa Mawu Othela Omwe Amuna Okhulupilika Anakamba
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2024
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 March tsa. 15

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Zisankho Zimene Zimaonetsa Kuti Timadalila Yehova

Tsiku lililonse timafunika kupanga zisankho zambili. Nthawi zambili anthu m’dzikoli amangotsatila zofuna za mtima wawo popanga zisankho, kapena amangotsatila khamu la anthu. (Eks. 23:2; Miy. 28:26) Koma amene amadalila Yehova, amam’kumbukila iye mwa kutsatila mfundo za m’Baibo popanga zisankho zawo.—Miy. 3:5, 6.

Kodi lemba lililonse pa malemba ali m’munsimu lingakuthandizeni kupanga cisankho pa cocitika monga citi? Lembani mayankho anu.

  • Mat. 6:33

  • Aroma 12:18

  • 1 Akor. 10:24

  • Aef. 5:15, 16

  • 1 Tim. 2:9, 10

  • Aheb. 13:5

ONELELANI VIDIYO YAKUTI TENGELANI CITSANZO CA ANTHU A CIKHULUPILILO OSATI OPANDA CIKHULUPILILO—MOSE, OSATI FARAO, KENAKO YANKHANI FUNSO ILI:

Cithunzi coonetsa zocitika za m’vidiyo yakuti “Tengelani Citsanzo ca Anthu a Cikhulupililo Osati Opanda Cikhulupililo—Mose, Osati Farao.” Pamene m’bale akupita ku msonkhano wacigawo, walandila foni ya ku nchito yomuuza zinthu zofuna cisamalilo ca mwamsanga.

Kodi citsanzo ca m’Baibo cinamuthandiza bwanji m’baleyu kupanga cisankho cabwino?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani