LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 May tsa. 2
  • Muziona Ena Mmene Yehova Amawaonela

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Muziona Ena Mmene Yehova Amawaonela
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • “Khulupililani Yehova Mulungu Wanu”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Yehosafati Adalila Yehova
    Buku Langa La Nkhani Za M’baibo
  • Yehova Anateteza Yehosafati
    Maphunzilo Amene Tingatengemo m’Baibo
  • Kodi Mudzatengelapo Phunzilo pa Zimene Zinalembedwa?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2017
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 May tsa. 2

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Muziona Ena Mmene Yehova Amawaonela

Mopanda nzelu, Mfumu Yehosafati inacita mgwilizano na Mfumu Ahabu (2 Mbiri 18:1-3; w17.03 24 ¶7)

Yehova anatuma Yehu kuti akadzudzule Yehosafati (2 Mbiri 19:1, 2)

Yehova anakumbukila zinthu zabwino zimene Yehosafati anacita (2 Mbiri 19:3; w15 8/15 11-12 ¶8-9)

M’bale wakhumudwa poona kuti m’bale wina akuceza mosangalala na tate komanso mwana wake m’malo moyeletsa m’Nyumba ya Ufumu.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Potengela citsanzo ca Yehova, kodi nimaona zabwino mwa ena m’malo moganizila cabe zophophonya zawo?’

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani