LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 November tsa. 16
  • Makonzedwe Olimbikitsa Atumiki a pa Beteli

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Makonzedwe Olimbikitsa Atumiki a pa Beteli
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Zisankho Zimene Zimaonetsa Kuti Timadalila Yehova
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Sitinakhalepo Tokha Ngakhale Pang’ono
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2025
  • Muzikumbukila Kuti Yehova ni “Mulungu Wamoyo”
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2024
  • Muzivomeleza Kuti Pali Zimene Simudziwa
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2025
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 November tsa. 16

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Makonzedwe Olimbikitsa Atumiki a pa Beteli

Munthu aliyense amakumana na mayeselo, ndipo amafunikila citonthozo na cilimbikitso. Ngakhale aja olimba mwauzimu, kapena amene ali na mautumiki apadela nawonso angalefuke. (Yobu 3:​1-3; Sal. 34:19) Kodi tingaphunzilepo ciyani pa makonzedwe olimbikitsa a m’banja la Beteli?

TAMBANI VIDIYO YAKUTI “DALILANI MULUNGU,” KENAKO YANKHANI MAFUNSO OTSATILAWA:

  • Kodi a m’banja la Beteli amakumana na mavuto otani?

  • Ni zinthu zinayi ziti zimene abale amacita poŵatonthoza?

  • Nanga abale amene amatonthoza ena amapindula bwanji?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani