UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Cifukwa Cake Kuonelela Zamalisece N’koipa
Masiku ano, zamalisece zili paliponse ndipo n’zosavuta kupeza. Anthu ambili, ngakhale opembedza amaona kuti kutamba zamalisece kulibe vuto.
TAMBANI VIDIYO YAKUTI KODI KUONELELA ZAMALISECE N’KUCIMWILA MULUNGU? KENAKO YANKHANI FUNSO ILI:
Kodi malemba awa amatithandiza bwanji kumvetsa mmene Mulungu amaonela zamaliseche?
-
-
Akol. 3:5
Yak. 1:14, 15