Jason Worilds: Ukamatumikila Yehova Umangopambana Basi
Pamene Jason anali kucita bwino kwambili m’masewela a mpila, anasankha kuleka masewelawo n’kuika patsogolo kutumikila Yehova.
Palibe vidiyo yake.
Pepani, vidiyo yakanga kulila.