Zamkati
Kodi Mungakonde Nkhani Iti Apa?
1 Kodi uthenga wabwino n’ciani?
3 Kodi uthenga wabwino ni wocokeladi kwa Mulungu?
5 Kodi Mulungu ali nalo colinga canji dziko lapansi?
6 Kodi tili ndi ciyembekezo canji ponena za akufa?
7 Kodi Ufumu wa Mulungu n’ciani?
8 N’cifukwa ciani Mulungu amalolela kuti anthu azivutika?
9 Mungacite ciani kuti banja lanu likhale lacimwemwe?
10 Kodi kulambila koona mungakudziŵe bwanji?
11 Kodi mfundo za m’Baibo zimatithandiza bwanji?
12 Kodi mungamuyandikile bwanji Mulungu?
13 Kodi uthenga wabwino wonena za cipembedzo ndi uti?
14 N’cifukwa ciani Mulungu ali ndi gulu?
15 N’cifukwa Ciani Muyenela Kupitiliza Kuphunzila za Yehova?