LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • sjj nyimbo 2
  • Dzina Lanu Ndimwe Yehova

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Dzina Lanu Ndimwe Yehova
  • ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Nkhani Zofanana
  • Dzina Lanu Ndimwe Yehova
    Imbilani Yehova—Nyimbo Zatsopano
  • Khalani ndi Moyo Wopambana
    Imbirani Yehova
  • Aphunzitseni Kucilimika
    ‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
  • Aphunzitseni Kucilimika
    Imbilani Yehova—Nyimbo Zatsopano
Onaninso Zina
‘Imbani Mokweza ndi Mosangalala’ kwa Yehova
sjj nyimbo 2

NYIMBO 2

Dzina Lanu Ndimwe Yehova

Yopulinta

(Salimo 83:18)

  1. 1. Mulungu woona—

    Wacilengedwe conse,

    Imwe ndimwe Yehova—

    Ku mibadwo yonse.

    Ndise onyadila

    Kukhala mpingo wanu.

    Tilengeza za imwe,

    Ku mitundu yonse.

    (KOLASI)

    Yehova, Yehova,

    Ndimwe M’lungu mwekha

    Kumwambako na padziko

    Kulibenso wina.

    Mulungu wamphamvu zonse

    Titamanda imwe.

    Yehova, Yehova,

    M’lungu wathu ndimwe mwekha.

  2. 2. Ise timakhala

    Ciliconse mufuna.

    Mwa cifunilo canu—

    Sitimalephela

    Mwatipatsa dzina;

    Tichedwa Mboni zanu

    Uyu ni mwayi wathu—

    Ndise anthu anu.

    (Kolasi)

    Yehova, Yehova,

    Ndimwe M’lungu mwekha

    Kumwambako na padziko

    Kulibenso wina.

    Mulungu wamphamvu zonse

    Titamanda imwe.

    Yehova, Yehova,

    M’lungu wathu ndimwe mwekha.

(Onaninso 2 Mbiri 6:14; Sal. 72:19; Yes. 42:8.)

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani