LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • km 6/13 tsa. 3
  • Kubweleza za M’sukulu ya Ulaliki

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kubweleza za M’sukulu ya Ulaliki
  • Utimiki Wathu wa Ufumu—2013
Utimiki Wathu wa Ufumu—2013
km 6/13 tsa. 3

Kubweleza za M’sukulu ya Ulaliki

Tidzakambilana mafunso otsatilawa pa Sukulu ya Ulaliki mkati mwa mlungu wa June 24, 2013. Taonetsa deti la mlungu umene tidzaphunzila mfundo iliyonse. Tacita zimenezi kuti mlungu uliwonse tizitha kufufuza mfundozo pokonzekela.

1. Kodi Yesu anatanthauzanji pamene ananena mau opezeka pa Yohane 3:14, 15 kuti: “Monga mmene Mose anakwezela njoka m’mwamba m’cipululu, momwemonso Mwana wa munthu ayenela kukwezedwa m’mwamba”? [May 6, w04 8/1 mas. 25, ndime 6

2. Kodi otsatila Kristu amalandila liti moyo mwa io okha, kapena kuloŵa m’moyo wokwanila? (Yoh. 6:53) [May 13, w03 9/15 tsa. 31 ndime 3]

3. Fotokozani citsanzo cimene Yesu anagwilitsila nchito kuti athandize anthu kudziŵa atate ake. (Yoh. 8:28) [May 20, w11 4/1 tsa. 7 ndime 3]

4. Kodi tiphunzilapo ciani pamene Yesu “anagwetsa misozi” bwenzi lake Lazaro atamwalila? (Yoh. 11:35) [May 20, w08 5/1 tsa. 24 ndime 3 mpaka 5]

5. Kodi Yesu anapeleka phunzilo lamphamvu liti pamene anasambitsa mapazi a ophunzila ake? (Yoh. 13:4, 5) [May 27, w99 3/1 tsa. 31 ndime 1]

6. Kodi mzimu wa Mulungu ungakhale bwanji mthandizi weni-weni kwa ife? (Yoh. 14:26) [May 27, w11 12/15 tsa. 15 ndime 9]

7. Kodi mau akuti “izi,” opezeka pa Yohane 21:15 atanthauzanji, ndipo tiphunzilapo ciani? [June 3, w08 4/15 tsa. 32 ndime 11]

8. Malinga ndi Machitidwe 2:44-47 ndi Machitidwe 4:34, 35, kodi ndi mzimu uti umene Akristu ayenela kutsatila? [June 10, w08 5/15 tsa. 30 ndime 5]

9. Kodi nkhani ya pa Machitidwe 7:59 imasonyeza kuti Sitefano anali kupemphela kwa Yesu? [June 17, w08 5/15 tsa. 31 ndime 2]

10. Kodi tingatsanzile bwanji citsanzo cabwino ca Baranaba, ndipo tidzapeza mapindu ati tikacita zimenezi? (Mac. 9:26, 27) [June 24, bt tsa. 65 ndime 19]

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani