Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Levitiko 7:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Iye azibweretsa yekha mafuta+ pamodzi ndi chidale ngati nsembe yowotcha pamoto yoperekedwa kwa Yehova. Ndipo aziyendetsa zinthu zimenezi uku ndi uku monga nsembe yoyendetsa uku ndi uku+ yoperekedwa kwa Yehova.

  • Numeri 8:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Choncho Aleviwo anadziyeretsa nʼkuchapa zovala zawo.+ Pambuyo pake, Aroni anawapereka kwa Yehova monga nsembe yoyendetsa uku ndi uku.+ Kenako Aroniyo anawaphimbira machimo awo kuti awayeretse.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani