Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Numeri 13:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Kenako Kalebe anayesa kukhazika anthuwo mtima pansi pamaso pa Mose ponena kuti: “Tiyeni tipite pompano, tikatenga dzikolo kukhala lathu, chifukwa tingathe kuwagonjetsa anthuwo.”+

  • Numeri 26:65
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 65 Zinakhala choncho chifukwa ponena za iwo, Yehova anati: “Ndithu anthu amenewa adzafera mʼchipululu.”+ Choncho, palibe amene anatsala kupatulapo Kalebe mwana wa Yefune ndi Yoswa mwana wa Nuni.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani