Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Ekisodo 23:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Levitiko 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Mukamapereka kwa Yehova nsembe yambewu ya zipatso zoyambirira kucha, muzipereka tirigu watsopano* wokazinga pamoto, wosinja kuti akhale nsembe yambewu ya zipatso zanu zoyambirira kucha.+

  • Numeri 18:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Numeri 18:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndakupatsa+ mafuta onse abwino koposa, vinyo yense watsopano wabwino koposa ndi mbewu zabwino koposa, zimenezi ndi zipatso zawo zoyambirira+ zimene azipereka kwa Yehova.

  • Deuteronomo 26:1, 2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 “Mukakalowa mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti likhale cholowa chanu, ndipo mukakalitengadi nʼkumakhalamo, 2 mukatenge zina mwa zipatso zoyambirira pa zokolola* zonse zamʼmunda mwanu zimene mudzakolole mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani. Mukaziike mʼdengu nʼkupita nazo kumalo amene Yehova Mulungu wanu adzasankhe kuika dzina lake.+

  • Miyambo 3:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani