Numeri 12:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano Miriamu ndi Aroni anayamba kumunena Mose chifukwa cha mkazi wa Chikusi+ amene anamukwatira. 2 Iwo ankanena kuti: “Kodi Yehova walankhula kudzera mwa Mose yekha? Kodi sanalankhulenso kudzera mwa ife?”+ Koma Yehova ankamvetsera.+ Numeri 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Salimo 106:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mumsasa, iwo anayamba kuchitira nsanje MoseNdiponso Aroni,+ woyera wa Yehova.+
12 Tsopano Miriamu ndi Aroni anayamba kumunena Mose chifukwa cha mkazi wa Chikusi+ amene anamukwatira. 2 Iwo ankanena kuti: “Kodi Yehova walankhula kudzera mwa Mose yekha? Kodi sanalankhulenso kudzera mwa ife?”+ Koma Yehova ankamvetsera.+