Numeri 31:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pajatu akazi amenewa ndi amene anatsatira mawu a Balamu nʼkunyengerera Aisiraeli kuti achimwire Yehova+ pa zimene zinachitika ku Peori,+ moti mliri unagwera gulu la anthu a Yehova.+ 1 Akorinto 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Chivumbulutso 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
16 Pajatu akazi amenewa ndi amene anatsatira mawu a Balamu nʼkunyengerera Aisiraeli kuti achimwire Yehova+ pa zimene zinachitika ku Peori,+ moti mliri unagwera gulu la anthu a Yehova.+