Deuteronomo 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova Mulungu wanu akadzawathamangitsa pamaso panu musadzanene mumtima mwanu kuti, ‘Yehova watilowetsa mʼdziko lino kuti tilitenge kukhala lathu, chifukwa chakuti ndife olungama.’+ Mʼmalomwake, Yehova akuthamangitsa mitundu iyi pamaso panu chifukwa choti ndi yoipa.+ Deuteronomo 32:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yesuruni* atanenepa, anapandukira mbuye wake. Iwe wanenepa, wakula thupi, wakhuta mopitirira muyezo.+ Choncho iye anasiya Mulungu amene anamupanga,+Ndipo ananyoza Thanthwe la chipulumutso chake.
4 Yehova Mulungu wanu akadzawathamangitsa pamaso panu musadzanene mumtima mwanu kuti, ‘Yehova watilowetsa mʼdziko lino kuti tilitenge kukhala lathu, chifukwa chakuti ndife olungama.’+ Mʼmalomwake, Yehova akuthamangitsa mitundu iyi pamaso panu chifukwa choti ndi yoipa.+
15 Yesuruni* atanenepa, anapandukira mbuye wake. Iwe wanenepa, wakula thupi, wakhuta mopitirira muyezo.+ Choncho iye anasiya Mulungu amene anamupanga,+Ndipo ananyoza Thanthwe la chipulumutso chake.