Numeri 35:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Aliyense amene wapha munthu aziphedwa+ pambuyo poti mboni zatsimikizira.+ Koma munthu sakuyenera kuphedwa ngati pali umboni woperekedwa ndi munthu mmodzi yekha. Deuteronomo 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mboni imodzi si yokwanira kutsimikizira kuti munthu wachitadi cholakwa kapena tchimo lililonse.+ Muzitsimikizira nkhaniyo mutamva umboni wochokera kwa* mboni ziwiri kapena zitatu.+
30 Aliyense amene wapha munthu aziphedwa+ pambuyo poti mboni zatsimikizira.+ Koma munthu sakuyenera kuphedwa ngati pali umboni woperekedwa ndi munthu mmodzi yekha.
15 Mboni imodzi si yokwanira kutsimikizira kuti munthu wachitadi cholakwa kapena tchimo lililonse.+ Muzitsimikizira nkhaniyo mutamva umboni wochokera kwa* mboni ziwiri kapena zitatu.+