Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Deuteronomo 20:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “Mukapita kunkhondo kukamenyana ndi adani anu, nʼkuona kuti ali ndi mahatchi, magaleta ankhondo komanso asilikali ochuluka kuposa inu, musachite nawo mantha chifukwa Yehova Mulungu wanu, amene anakutulutsani mʼdziko la Iguputo ali ndi inu.+

  • 2 Samueli 8:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Davide anagwira amuna 1,700 okwera pamahatchi ndi asilikali 20,000 oyenda pansi a Hadadezeri. Kenako Davide anapundula* mahatchi onse a magaleta nʼkungosiya mahatchi 100.+

  • Salimo 20:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Ena amadalira magaleta ndipo ena amadalira mahatchi,+

      Koma ife timadalira dzina la Yehova Mulungu wathu.+

  • Miyambo 21:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani