-
Salimo 125:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Koma anthu amene apatuka panjira yabwino nʼkuyamba kuyenda mʼnjira zokhotakhota,
Yehova adzawachotsa limodzi ndi anthu ochita zoipa.+
Mu Isiraeli mukhale mtendere.
-