-
2 Samueli 15:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Anthu onse amʼdzikoli ankalira mokweza mawu, pamene anthu onse amene anali ndi Davide ankadutsa. Mfumu inali itaimirira pafupi ndi chigwa cha Kidironi+ ndipo anthu onse ankawoloka kulowera kumsewu wopita kuchipululu.
-