-
Deuteronomo 28:38Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
38 Mudzadzala mbewu zambiri mʼmunda, koma mudzakolola zochepa+ chifukwa dzombe lidzadya mbewuzo.