-
Levitiko 25:42Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
42 Aisiraeli ndi akapolo anga amene ndinawatulutsa mʼdziko la Iguputo.+ Choncho asamadzigulitse ngati mmene anthu amagulitsira kapolo.
-
-
Deuteronomo 5:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Muzikumbukira kuti munali akapolo mʼdziko la Iguputo ndipo Yehova Mulungu wanu anakutulutsani kumeneko ndi dzanja lamphamvu komanso mkono wotambasula.+ Nʼchifukwa chake Yehova Mulungu wanu anakulamulani kuti muzisunga tsiku la Sabata.
-