Nehemiya 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Awa ndi mawu a Nehemiya*+ mwana wa Hakaliya. Mʼmwezi wa Kisilevi,* mʼchaka cha 20, ine ndinali kunyumba ya mfumu yokhala ndi mpanda wolimba kwambiri ya ku Susani.*+
1 Awa ndi mawu a Nehemiya*+ mwana wa Hakaliya. Mʼmwezi wa Kisilevi,* mʼchaka cha 20, ine ndinali kunyumba ya mfumu yokhala ndi mpanda wolimba kwambiri ya ku Susani.*+