-
Numeri 18:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Zipatso zonse zoyamba kupsa mʼminda yawo, zimene azizipereka kwa Yehova zizikhala zako.+ Aliyense wamʼnyumba yako amene si wodetsedwa angathe kudya nawo.
-