-
Numeri 15:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Muzikapereka mikate yozungulira yoboola pakati ya ufa wamisere kuti ikhale chopereka cha zipatso zoyambirira kucha.+ Muzikaipereka ngati mmene mumaperekera chopereka chochokera popunthira mbewu.
-