Nehemiya 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yesuwa anabereka Yoyakimu, Yoyakimu anabereka Eliyasibu,+ Eliyasibu anabereka Yoyada.+ Nehemiya 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Nehemiya 13:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mmodzi mwa ana aamuna a Yoyada,+ mwana wa Eliyasibu,+ mkulu wa ansembe anali mkamwini wa Sanibalati+ wa ku Beti-horoni. Choncho ndinamuthamangitsa.
28 Mmodzi mwa ana aamuna a Yoyada,+ mwana wa Eliyasibu,+ mkulu wa ansembe anali mkamwini wa Sanibalati+ wa ku Beti-horoni. Choncho ndinamuthamangitsa.