-
Yobu 3:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Nʼchifukwa chiyani Mulungu amapereka kuwala kwa munthu amene wasochera,
Amene Mulungu wamutchingira njira?+
-
-
Salimo 88:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Anzanga mwawathamangitsira kutali ndi ine.+
Mwandipangitsa kuti ndikhale chinthu chonyansa kwa iwo.
Ndakodwa ndipo sindingathe kuthawa.
-