-
Yobu 12:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Iye akagwetsa chinthu, sichingamangidwenso,+
Zimene iye watseka, palibe munthu amene angatsegule.
-
-
Yobu 19:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Iye watseka njira yanga ndi khoma lamiyala moti sindingathe kudutsa,
Watchinga njira zanga ndi mdima.+
-