Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yobu 5:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Yobu 26:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Yobu 37:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pogwiritsa ntchito mpweya wake Mulungu amapangitsa kuti madzi aundane,+

      Komanso kuti madzi aundane chifukwa cha kuzizira.+

  • Salimo 135:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Miyambo 30:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Ndi ndani amene anakwerapo kumwamba kenako nʼkutsika?+

      Ndi ndani amene anasonkhanitsapo mphepo mʼmanja mwake?

      Ndi ndani amene anamangapo madzi pachovala chake?+

      Ndi ndani amene anaika malire a dziko lapansi?+

      Dzina lake ndi ndani, nanga mwana wake dzina lake ndi ndani? Ndiuzeni ngati mukudziwa.

  • Yesaya 40:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndi ndani anayezapo madzi onse amʼnyanja pachikhatho cha dzanja lake?+

      Ndi ndani anayezapo kumwamba ndi dzanja lake?

      Ndi ndani anasonkhanitsapo fumbi lonse lapadziko lapansi mʼmbale yoyezera+

      Kapena kuyeza mapiri pachoyezera

      Komanso zitunda pasikelo?

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani