Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 1 Mafumu 18:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Yobu 36:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Kodi alipo amene angamvetse mmene mitambo anaitambasulira,

      Komanso kugunda kochokera mutenti yake?*+

  • Yobu 36:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Pogwiritsa ntchito zimenezi, iye amapereka chakudya kwa anthu onse.

      Amawapatsa chakudya chochuluka.+

  • Yobu 38:25-27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndi ndani anatsegula ngalande za madzi a mvula kuthambo,

      Nʼkupanga njira ya mtambo wa mvula yamabingu,+

      26 Kuti achititse mvula kugwa kumalo amene sikukhala munthu,

      Kuchipululu kumene kulibe anthu,+

      27 Kuti inyowetse chipululu chouma chomwe ndi chowonongeka,

      Nʼkuchititsa kuti udzu umere?+

  • Yakobo 5:17, 18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani