- 
	                        
            
            Yeremiya 51:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
- 
                            - 
                                        35 Anthu amene akukhala mu Ziyoni akunena kuti, ‘Chiwawa chimene anachitira ine ndi thupi langa chigwerenso Babulo.’+ Ndipo Yerusalemu akunena kuti, ‘Magazi anga akhale pa anthu amene akukhala mʼdziko la Kasidi.’” 
 
-