-
Salimo 71:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Mukhale thanthwe langa lachitetezo
Loti ndizilowamo nthawi zonse.
Lamulani kuti ndipulumutsidwe,
Chifukwa inu ndinu thanthwe langa ndi malo anga achitetezo.+
-
-
Salimo 90:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
90 Inu Yehova, mwakhala malo athu okhalamo+ ku mibadwo yonse.
-