-
Numeri 27:13, 14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ukaliona dzikolo, iwenso udzaikidwa mʼmanda ngati mmene anachitira ndi makolo ako*+ komanso Aroni mchimwene wako,+ 14 chifukwa pamene gulu lija linakangana nane mʼchipululu cha Zini, inu munapandukira mawu anga ndipo munalephera kundilemekeza pamaso pa gululo pamadzi+ a Meriba+ ku Kadesi,+ mʼchipululu cha Zini.”+
-