Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Ekisodo 14:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Numeri 11:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Kenako Yehova anabweretsa mphepo yamphamvu kuchokera kunyanja. Mphepoyo inabweretsa zinziri, ndipo inazimwaza kuzungulira msasawo+ mpaka pamtunda woyenda tsiku limodzi kulowera mbali zonse za msasawo. Inazimwaza kuzungulira msasawo, moti zinaunjikana mulu wokwana pafupifupi masentimita 90* kuchokera pansi.

  • Yeremiya 10:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Mawu ake akamveka,

      Madzi akumwamba amachita mkokomo,+

      Ndipo amachititsa mitambo* kukwera kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+

      Iye amachititsa kuti kukamagwa mvula mphezi zizingʼanima,

      Ndipo amatulutsa mphepo mʼnyumba zake zosungira.+

  • Yeremiya 51:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Mawu ake akamveka,

      Madzi akumwamba amachita mkokomo,

      Ndipo amachititsa mitambo* kukwera kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.

      Iye amachititsa kuti kukamagwa mvula mphezi zizingʼanima

      Ndipo amatulutsa mphepo mʼnyumba zake zosungira.+

  • Yona 1:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndiyeno Yehova anabweretsa mphepo yamphamvu panyanja, ndipo kenako panachitika chimkuntho choopsa, moti chombocho chinatsala pangʼono kusweka.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani