-
Yeremiya 49:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Ponena za Edomu, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti:
“Kodi nzeru zinatha ku Temani?+
Kodi anthu ozindikira sakuperekanso malangizo anzeru?
Kodi nzeru zawo zinawola?
-
-
Ezekieli 25:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Edomu wabwezera zoipa kwa nyumba ya Yuda ndipo wapalamula mlandu waukulu chifukwa chowabwezera.+
-