-
Salimo 71:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ndakhala ndikudalira inu kuchokera tsiku limene ndinabadwa.
Inu ndi amene munanditulutsa mʼmimba mwa mayi anga.+
Ndimakutamandani nthawi zonse.
-