Salimo 104:27, 28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Zonsezi zimayembekezera inuKuti muzipatse chakudya pa nyengo yake.+ 28 Zimasonkhanitsa zimene mwazipatsa.+ Mukatambasula dzanja lanu, zimakhutira ndi zinthu zabwino.+ Salimo 107:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Salimo 132:14, 15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Awa ndi malo anga okhalamo mpaka kalekale.Ndidzakhala mmenemu,+ chifukwa zimenezi ndi zimene ndikulakalaka. 15 Ndidzadalitsa kwambiri malo amenewa ndi chakudya.Anthu ake osauka ndidzawapatsa chakudya chokwanira.+
27 Zonsezi zimayembekezera inuKuti muzipatse chakudya pa nyengo yake.+ 28 Zimasonkhanitsa zimene mwazipatsa.+ Mukatambasula dzanja lanu, zimakhutira ndi zinthu zabwino.+
14 “Awa ndi malo anga okhalamo mpaka kalekale.Ndidzakhala mmenemu,+ chifukwa zimenezi ndi zimene ndikulakalaka. 15 Ndidzadalitsa kwambiri malo amenewa ndi chakudya.Anthu ake osauka ndidzawapatsa chakudya chokwanira.+