Genesis 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Salimo 104:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mukabisa nkhope yanu, zimasokonezeka. Mukachotsa mzimu wawo,* zimafa ndipo zimabwerera kufumbi.+ Mlaliki 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Mlaliki 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako fumbi lidzabwerera kunthaka+ kumene linali, ndipo mzimu* udzabwerera kwa Mulungu woona amene anaupereka.+
7 Kenako fumbi lidzabwerera kunthaka+ kumene linali, ndipo mzimu* udzabwerera kwa Mulungu woona amene anaupereka.+