Yobu 19:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ine ndikudziwa bwino kuti wondiwombola+ ali moyo,Iye adzabwera nthawi ina ndipo adzaimirira padziko lapansi.* Yesaya 43:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova, Wokuwombolani,+ Woyera wa Isiraeli,+ wanena kuti: “Chifukwa cha inu, ndidzatumiza asilikali ku Babulo ndipo adzagwetsa zotsekera mʼmageti,+Komanso Akasidi adzalira chifukwa chopanikizika, ali mʼsitima zawo zapamadzi.+
25 Ine ndikudziwa bwino kuti wondiwombola+ ali moyo,Iye adzabwera nthawi ina ndipo adzaimirira padziko lapansi.*
14 Yehova, Wokuwombolani,+ Woyera wa Isiraeli,+ wanena kuti: “Chifukwa cha inu, ndidzatumiza asilikali ku Babulo ndipo adzagwetsa zotsekera mʼmageti,+Komanso Akasidi adzalira chifukwa chopanikizika, ali mʼsitima zawo zapamadzi.+