-
Salimo 118:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Nditsegulireni mageti achilungamo.+
Ndidzalowa mmenemo ndipo ndidzatamanda Ya.
-
-
Salimo 122:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Ndipo tsopano mapazi athu aima
Pamageti ako iwe Yerusalemu.+
-