-
Yesaya 12:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Pa tsiku limenelo ndithu udzanena kuti:
“Ndikukuthokozani, inu Yehova
Chifukwa ngakhale munandikwiyira,
Mkwiyo wanu unachepa pangʼonopangʼono ndipo munanditonthoza.+
-