2 Mafumu 7:6, 7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Salimo 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ena amadalira magaleta ndipo ena amadalira mahatchi,+Koma ife timadalira dzina la Yehova Mulungu wathu.+ Miyambo 21:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Yesaya 31:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Tsoka kwa anthu amene amapita ku Iguputo kukapempha thandizo,+Amene amadalira mahatchi,+Amene amadalira magaleta ankhondo chifukwa chakuti ndi ambiri,Komanso mahatchi ankhondo* chifukwa chakuti ndi amphamvu kwambiri. Koma sayangʼana kwa Woyera wa Isiraeli,Ndipo safunafuna Yehova.
7 Ena amadalira magaleta ndipo ena amadalira mahatchi,+Koma ife timadalira dzina la Yehova Mulungu wathu.+
31 Tsoka kwa anthu amene amapita ku Iguputo kukapempha thandizo,+Amene amadalira mahatchi,+Amene amadalira magaleta ankhondo chifukwa chakuti ndi ambiri,Komanso mahatchi ankhondo* chifukwa chakuti ndi amphamvu kwambiri. Koma sayangʼana kwa Woyera wa Isiraeli,Ndipo safunafuna Yehova.