Yesaya 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Phunzirani kuchita zabwino, muzichita chilungamo,+Dzudzulani munthu wopondereza ena,Tetezani ufulu wa mwana wamasiye,Ndipo muteteze mkazi wamasiye pa mlandu wake.”+ Aheberi 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
17 Phunzirani kuchita zabwino, muzichita chilungamo,+Dzudzulani munthu wopondereza ena,Tetezani ufulu wa mwana wamasiye,Ndipo muteteze mkazi wamasiye pa mlandu wake.”+