Yobu 24:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Oipawo amakhala okwezeka kwa kanthawi, kenako nʼkutha.+ Iwo ali ngati ngala za tirigu zimene zimadulidwa nʼkuikidwa pamodzi.Amatsitsidwa+ ndipo amafa mofanana ndi anthu ena onse.
24 Oipawo amakhala okwezeka kwa kanthawi, kenako nʼkutha.+ Iwo ali ngati ngala za tirigu zimene zimadulidwa nʼkuikidwa pamodzi.Amatsitsidwa+ ndipo amafa mofanana ndi anthu ena onse.