Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • 2 Mafumu 5:20-22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Gehazi,+ mtumiki wa Elisa munthu wa Mulungu woona,+ anaganiza mumtima mwake kuti: ‘Zoona mbuyanga wangomusiya Namani wa ku Siriya+ uja osalandira zinthu zomwe anabweretsa? Ndikulumbira mʼdzina la Yehova Mulungu wamoyo, ndimʼthamangira kuti ndikatengeko zinthu zina.’ 21 Gehazi anathamangiradi Namani ndipo Namani ataona kuti munthu akumʼthamangira, anatsika pagaleta lake kuti akumane naye. Kenako anati: “Nʼkwabwino?” 22 Gehazi anayankha kuti: “Inde nʼkwabwino. Mbuyanga wandituma kuti, ‘Posachedwapa kwabwera anyamata awiri, ana a aneneri, kuchokera kudera lamapiri la Efuraimu. Muwapatseko talente imodzi ya siliva ndi zovala ziwiri.’”+

  • Yeremiya 17:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Munthu amene amapeza chuma mwachinyengo,*+

      Ali ngati nkhwali imene imasonkhanitsa mazira amene sinaikire.

      Chuma chakecho chidzatha asanakwanitse hafu ya zaka za moyo wake,

      Ndipo pamapeto pake adzadziwika kuti ndi wopusa.”

  • 1 Timoteyo 6:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani