Miyambo 28:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Munthu wokhulupirika adzalandira madalitso ambiri,+Koma amene akufuna kulemera mofulumira, sadzapitiriza kukhala wosalakwa.+ Yesaya 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Akalonga ako ndi osamva ndipo amagwirizana ndi anthu akuba.+ Aliyense wa iwo amakonda ziphuphu ndipo amalakalaka kupatsidwa mphatso.+ Mwana wamasiye samuweruza mwachilungamo,Ndipo ngakhale mlandu wa mkazi wamasiye safuna kuuweruza.+ Yakobo 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
20 Munthu wokhulupirika adzalandira madalitso ambiri,+Koma amene akufuna kulemera mofulumira, sadzapitiriza kukhala wosalakwa.+
23 Akalonga ako ndi osamva ndipo amagwirizana ndi anthu akuba.+ Aliyense wa iwo amakonda ziphuphu ndipo amalakalaka kupatsidwa mphatso.+ Mwana wamasiye samuweruza mwachilungamo,Ndipo ngakhale mlandu wa mkazi wamasiye safuna kuuweruza.+