-
Nyimbo ya Solomo 1:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 “Undikise ndi milomo yako,
Chifukwa chikondi chimene umandisonyeza chimaposa vinyo.+
-
-
Nyimbo ya Solomo 4:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Chikondi chimene umandisonyeza nʼchokoma,+ iwe mchemwali wanga, mkwatibwi wanga.
-