1 Mafumu 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mahatchi a Solomo ankawagula kuchokera ku Iguputo ndipo gulu la amalonda a mfumu linkagula mahatchiwo mʼmagulumagulu.*+ 2 Mbiri 1:16, 17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Nyimbo ya Solomo 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Wokondedwa wangawe,+ ndiwe wokongola ngati Tiriza,*+Ndiwe wooneka bwino ngati Yerusalemu,+Ndipo ndiwe wogometsa ngati magulu a asilikali amene azungulira mbendera.+
28 Mahatchi a Solomo ankawagula kuchokera ku Iguputo ndipo gulu la amalonda a mfumu linkagula mahatchiwo mʼmagulumagulu.*+
4 “Wokondedwa wangawe,+ ndiwe wokongola ngati Tiriza,*+Ndiwe wooneka bwino ngati Yerusalemu,+Ndipo ndiwe wogometsa ngati magulu a asilikali amene azungulira mbendera.+