-
Yesaya 42:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Taonani, zinthu zimene ndinaneneratu kalekale zachitika,
Tsopano ndikulengeza zinthu zatsopano.
Zisanayambe kuonekera, ndimakuuzani.”+
-
-
Yesaya 48:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ine ndinakuuzani kalekale.
Zisanachitike nʼkomwe, ine ndinachititsa kuti muzimve,
Kuti musanene kuti, ‘Fano langa ndi limene linachita zimenezi.
Chifaniziro changa chosema komanso chifaniziro chachitsulo* nʼzimene zinalamula zimenezi.’
-