Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Yesaya 44:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kodi pali aliyense wopusa amene angafike popanga mulungu kapena fano lopangidwa ndi chitsulo chosungunula,*

      Lomwe ndi lopanda phindu?+

  • Yeremiya 10:14, 15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Munthu aliyense akuchita zinthu mopanda nzeru komanso mosazindikira.

      Mmisiri wa zitsulo aliyense adzachita manyazi chifukwa cha chifaniziro chake chosula.+

      Chifukwa chifaniziro chake chopangidwa ndi chitsulo chosungunula ndi mulungu wonama

      Ndipo mafano amenewa alibe mzimu.*+

      15 Iwo ndi achabechabe, oyenera kunyozedwa.+

      Tsiku loti aweruzidwe likadzafika adzawonongedwa.

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani