-
Yeremiya 51:28, 29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Sankhani* mitundu ya anthu kuti ichite naye nkhondo.
Sankhani mafumu a ku Mediya,+ abwanamkubwa ake ndi achiwiri kwa olamulira awo onse
Komanso mayiko onse amene iwo amawalamulira.
29 Dziko lidzagwedezeka ndi kunjenjemera,
Chifukwa Yehova adzachitira Babulo zimene akuganiza
Kuti dziko la Babulo likhale chinthu chochititsa mantha, lopanda munthu wokhalamo.+
-